Aroma 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musabwezere choipa pa choipa.+ Chitani zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino.