-
1 Atesalonika 5:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Amene akukuitanani ndi wokhulupirika, ndipo adzachitadi zimenezi.
-
-
2 Atesalonika 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pa chifukwa chimenechi, ndithu timakupemphererani nthawi zonse. Timatero kuti Mulungu wathu akuoneni kuti ndinu oyenereradi kuitanidwa ndi iye.+ Mulunguyo achite mokwanira zinthu zonse zabwino zimene akufuna kuchita ndi mphamvu zake, ndipo achititse kuti ntchito zanu zachikhulupiriro zikhale zopindulitsa,
-