Aroma 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mkwiyo wa Mulungu+ ukusonyezedwa kuchokera kumwamba pa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zosalungama+ amene akupondereza choonadi+ m’njira yosalungama.+
18 Mkwiyo wa Mulungu+ ukusonyezedwa kuchokera kumwamba pa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zosalungama+ amene akupondereza choonadi+ m’njira yosalungama.+