2 Atesalonika 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, Ambuye wathu Yesu Khristu mwiniyo, ndi Mulungu Atate wathu, amene anatikonda+ ndipo amatilimbikitsa m’njira yosalephera ndiponso anatipatsa chiyembekezo chabwino,+ mwa kukoma mtima kwakukulu,
16 Komanso, Ambuye wathu Yesu Khristu mwiniyo, ndi Mulungu Atate wathu, amene anatikonda+ ndipo amatilimbikitsa m’njira yosalephera ndiponso anatipatsa chiyembekezo chabwino,+ mwa kukoma mtima kwakukulu,