Mateyu 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 chifukwa ambiri adzabwera m’dzina langa ndi kunena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ ndipo adzasocheretsa anthu ambiri.+ 1 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+ 2 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzasiya kumvetsera choonadi, n’kutembenukira ku nkhani zonama.+
5 chifukwa ambiri adzabwera m’dzina langa ndi kunena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ ndipo adzasocheretsa anthu ambiri.+
4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+