1 Akorinto 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano ndikukuyamikirani chifukwa chakuti mukundikumbukira m’zinthu zonse, ndipo mukusunga miyambo+ monga mmene ndinaiperekera kwa inu.
2 Tsopano ndikukuyamikirani chifukwa chakuti mukundikumbukira m’zinthu zonse, ndipo mukusunga miyambo+ monga mmene ndinaiperekera kwa inu.