Machitidwe 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Inunso mukudziwa bwino kuti manja awa anagwira ntchito kuti ndipeze zosowa zanga+ ndi za amene ali nane.
34 Inunso mukudziwa bwino kuti manja awa anagwira ntchito kuti ndipeze zosowa zanga+ ndi za amene ali nane.