-
Machitidwe 28:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tsopano pafupi ndi malo amenewa, panali minda ya munthu woyang’anira chilumbacho, dzina lake Papuliyo. Iyeyu anatilandira ndi kutichereza bwino kwambiri masiku atatu.
-