Machitidwe 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mawu aja anamvekanso kwa iye kachiwiri kuti: “Zinthu zimene Mulungu waziyeretsa usiyiretu kuzinena kuti n’zoipitsidwa.”+
15 Ndipo mawu aja anamvekanso kwa iye kachiwiri kuti: “Zinthu zimene Mulungu waziyeretsa usiyiretu kuzinena kuti n’zoipitsidwa.”+