Machitidwe 27:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atanena zimenezi, anatenga mkate. Kenako anayamika+ kwa Mulungu pamaso pa onse n’kunyema mkatewo ndi kuyamba kudya.
35 Atanena zimenezi, anatenga mkate. Kenako anayamika+ kwa Mulungu pamaso pa onse n’kunyema mkatewo ndi kuyamba kudya.