Mateyu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+ Aroma 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+
33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+
28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+