Salimo 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kondani Yehova, inu nonse okhulupirika ake.+Yehova amateteza okhulupirika,+Koma aliyense wodzikuza adzamulanga mowirikiza.+
23 Kondani Yehova, inu nonse okhulupirika ake.+Yehova amateteza okhulupirika,+Koma aliyense wodzikuza adzamulanga mowirikiza.+