2 Timoteyo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 lalikira mawu.+ Lalikira modzipereka, m’nthawi yabwino+ ndi m’nthawi yovuta.+ Dzudzula,+ tsutsa, dandaulira. Chita zimenezi ndi luso la kuphunzitsa ndiponso moleza mtima kwambiri.+ Tito 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma iwe pitiriza kulankhula zinthu zogwirizana ndi chiphunzitso cholondola.+
2 lalikira mawu.+ Lalikira modzipereka, m’nthawi yabwino+ ndi m’nthawi yovuta.+ Dzudzula,+ tsutsa, dandaulira. Chita zimenezi ndi luso la kuphunzitsa ndiponso moleza mtima kwambiri.+