Aroma 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho, Chilamulo kumbali yake n’choyera,+ ndipo malamulo ndi oyera, olungama+ ndi abwino.+