1 Timoteyo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komabe, mkazi adzatetezeka mwa kubereka ana,+ malinga ngati akupitiriza kukhala ndi chikhulupiriro, chikondi, ndi kukhala woyera ndiponso woganiza bwino.+
15 Komabe, mkazi adzatetezeka mwa kubereka ana,+ malinga ngati akupitiriza kukhala ndi chikhulupiriro, chikondi, ndi kukhala woyera ndiponso woganiza bwino.+