2 Petulo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma angelo, ngakhale kuti ndi amphamvu kwambiri, saneneza aphunzitsi onyengawo ndi mawu onyoza,+ pakuti amalemekeza Yehova.+
11 Koma angelo, ngakhale kuti ndi amphamvu kwambiri, saneneza aphunzitsi onyengawo ndi mawu onyoza,+ pakuti amalemekeza Yehova.+