Miyambo 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wolemera amadziona ngati wanzeru m’maso mwake,+ koma munthu wonyozeka amene ali wozindikira zinthu amam’fufuza n’kudziwa zoona zake.+
11 Munthu wolemera amadziona ngati wanzeru m’maso mwake,+ koma munthu wonyozeka amene ali wozindikira zinthu amam’fufuza n’kudziwa zoona zake.+