Aheberi 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho, tiyeni tiyandikire mpando wachifumu wa kukoma mtima kwakukulu ndipo tipemphere kwa Mulungu+ ndi ufulu wa kulankhula,+ kuti atichitire chifundo ndi kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi imene tikufunika thandizo.+ 2 Yohane 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tidzalandira kukoma mtima kwakukulu,+ chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate+ wathu ndi kwa Yesu Khristu Mwana wa Atate, limodzi ndi choonadi ndiponso chikondi.+
16 Choncho, tiyeni tiyandikire mpando wachifumu wa kukoma mtima kwakukulu ndipo tipemphere kwa Mulungu+ ndi ufulu wa kulankhula,+ kuti atichitire chifundo ndi kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi imene tikufunika thandizo.+
3 Tidzalandira kukoma mtima kwakukulu,+ chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate+ wathu ndi kwa Yesu Khristu Mwana wa Atate, limodzi ndi choonadi ndiponso chikondi.+