Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aheberi 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma tsopano Yesu walandira ntchito yapamwamba kwambiri yotumikira ena, moti wakhalanso mkhalapakati+ wa pangano labwino kwambiri,+ limene lakhazikitsidwa mwalamulo pa malonjezo abwinonso.+

  • Aheberi 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chotero, ndiye chifukwa chake iye ali mkhalapakati+ wa pangano latsopano kuti anthu amene aitanidwa alandire lonjezo la cholowa chamuyaya.+ Izi zatheka chifukwa cha imfa yake, imene inali ngati dipo+ lawo lowamasula ku machimo amene iwo anali nawo m’pangano lakale lija.+

  • Aheberi 12:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi owaza,+ amene amalankhula m’njira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena