Aefeso 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipotu, monga mmene mpingo umagonjerera Khristu, akazinso agonjere amuna awo m’chilichonse.+