Genesis 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova Mulungu atamva zimenezi, anafunsa mkaziyo kuti: “Ndiye chiyani wachitachi?” Mkaziyo anayankha kuti: “Njoka ndi imene inandinyenga, ndipo ine ndadya.”+
13 Yehova Mulungu atamva zimenezi, anafunsa mkaziyo kuti: “Ndiye chiyani wachitachi?” Mkaziyo anayankha kuti: “Njoka ndi imene inandinyenga, ndipo ine ndadya.”+