Yohane 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake Machitidwe 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire+ kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira wakuti iyeyu ndi Amene Mulungu anamuika kukhala woweruza anthu amoyo ndi akufa.+
28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake
42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire+ kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira wakuti iyeyu ndi Amene Mulungu anamuika kukhala woweruza anthu amoyo ndi akufa.+