Machitidwe 2:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Anali kutamanda Mulungu ndipo anthu onse anali kuwakonda.+ Komanso tsiku ndi tsiku, Yehova anapitiriza kuwawonjezera+ anthu amene anali kuwapulumutsa.+ Aefeso 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 anatikhalitsa amoyo pamodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa m’machimo,+ (pakuti inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu)+
47 Anali kutamanda Mulungu ndipo anthu onse anali kuwakonda.+ Komanso tsiku ndi tsiku, Yehova anapitiriza kuwawonjezera+ anthu amene anali kuwapulumutsa.+
5 anatikhalitsa amoyo pamodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa m’machimo,+ (pakuti inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu)+