1 Timoteyo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithu Timoteyo, sunga bwino chimene chinaikidwa m’manja mwako.+ Pewa nkhani zopanda pake zimene zimaipitsa zinthu zoyera. Upewenso mitsutso pa zimene ena monama amati ndiye “kudziwa zinthu.”+
20 Ndithu Timoteyo, sunga bwino chimene chinaikidwa m’manja mwako.+ Pewa nkhani zopanda pake zimene zimaipitsa zinthu zoyera. Upewenso mitsutso pa zimene ena monama amati ndiye “kudziwa zinthu.”+