Afilipi 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu. 2 Timoteyo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zinthu zimene unazimva kwa ine ndi kwa mboni zambiri+ zokhudza ine, zimenezo uziphunzitse kwa anthu okhulupirika amene nawonso, adzakhala oyenerera bwino kuphunzitsa ena.+ 2 Timoteyo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iwe, pitiriza kutsatira zimene unaphunzira ndi zimene unakhulupirira pambuyo pokhutira nazo,+ chifukwa ukudziwa anthu amene anakuphunzitsa.+
9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu.
2 Zinthu zimene unazimva kwa ine ndi kwa mboni zambiri+ zokhudza ine, zimenezo uziphunzitse kwa anthu okhulupirika amene nawonso, adzakhala oyenerera bwino kuphunzitsa ena.+
14 Koma iwe, pitiriza kutsatira zimene unaphunzira ndi zimene unakhulupirira pambuyo pokhutira nazo,+ chifukwa ukudziwa anthu amene anakuphunzitsa.+