1 Timoteyo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwana wanga Timoteyo, ndikukulamulira+ kuchita izi malinga ndi maulosi+ amene ananeneratu za iwe, kuti mogwirizana ndi maulosiwo upitirize kumenya nkhondo yabwino.+
18 Mwana wanga Timoteyo, ndikukulamulira+ kuchita izi malinga ndi maulosi+ amene ananeneratu za iwe, kuti mogwirizana ndi maulosiwo upitirize kumenya nkhondo yabwino.+