Machitidwe 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Mulungu anamuukitsa+ kwa akufa mwa kumasula zopweteka za imfa,+ chifukwa zinali zosatheka kuti imfa ipitirize kumugwira mwamphamvu.+ 1 Akorinto 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiponso kuti anaikidwa m’manda,+ kenako anaukitsidwa+ tsiku lachitatu,+ mogwirizana ndi Malemba.+
24 Koma Mulungu anamuukitsa+ kwa akufa mwa kumasula zopweteka za imfa,+ chifukwa zinali zosatheka kuti imfa ipitirize kumugwira mwamphamvu.+