2 Timoteyo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 kuti munthu wa Mulungu akhale woyenerera bwino+ ndi wokonzeka mokwanira kuchita ntchito iliyonse yabwino.+ Tito 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera+ ndi kumvera maboma ndiponso olamulira.+ Komanso akhale okonzekera ntchito iliyonse yabwino.+
17 kuti munthu wa Mulungu akhale woyenerera bwino+ ndi wokonzeka mokwanira kuchita ntchito iliyonse yabwino.+
3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera+ ndi kumvera maboma ndiponso olamulira.+ Komanso akhale okonzekera ntchito iliyonse yabwino.+