Aroma 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti anthu oterowo si akapolo a Ambuye wathu Khristu, koma a mimba zawo.+ Ndipo mwa kulankhula mawu okopa+ ndi achinyengo+ amanyenga anthu oona mtima. 1 Timoteyo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu ena akana kutsatira zimenezi ndipo asocheretsedwa+ n’kuyamba kutsatira nkhani zopanda pake.+
18 Pakuti anthu oterowo si akapolo a Ambuye wathu Khristu, koma a mimba zawo.+ Ndipo mwa kulankhula mawu okopa+ ndi achinyengo+ amanyenga anthu oona mtima.