Agalatiya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anadzipereka chifukwa cha machimo athu,+ kuti atilanditse ku nthawi* yoipayi,+ mogwirizana ndi chifuniro+ cha Mulungu ndi Atate wathu. Aefeso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+ Akolose 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwa Mwana wakeyo, tinamasulidwa ndi dipo,* kutanthauza kuti machimo athu anakhululukidwa.+
4 Iye anadzipereka chifukwa cha machimo athu,+ kuti atilanditse ku nthawi* yoipayi,+ mogwirizana ndi chifuniro+ cha Mulungu ndi Atate wathu.
7 Kudzera mwa iyeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi+ ake, inde, takhululukidwa+ machimo athu, malinga ndi chuma cha kukoma mtima kwake kwakukulu.+