Salimo 95:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunena za anthu amenewa ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti:+“Sadzalowa mu mpumulo wanga.”+ Aheberi 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti, ‘Sadzalowa+ mu mpumulo wanga.’”+