Salimo 95:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunena za anthu amenewa ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti:+“Sadzalowa mu mpumulo wanga.”+