Malaki 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ine ndine Yehova, sindinasinthe.+ Inu ndinu ana a Yakobo ndipo simunatheretu.+