Yohane 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anamuyankha kuti: “Ifetu ndife ana a Abulahamu+ ndipo sitinakhalepo akapolo a munthu.+ Tsopano iwe ukunena bwanji kuti, ‘Mudzamasulidwa’?”
33 Iwo anamuyankha kuti: “Ifetu ndife ana a Abulahamu+ ndipo sitinakhalepo akapolo a munthu.+ Tsopano iwe ukunena bwanji kuti, ‘Mudzamasulidwa’?”