Yesaya 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Makamu onse akumwamba adzawola.+ Kumwamba kudzapindidwa ngati mpukutu wolembapo.+ Makamu onse akumwambawo adzafota ngati mmene masamba amafotera pamtengo wa mpesa n’kuthothoka, ndiponso ngati mmene nkhuyu yonyala imathothokera mumtengo wa mkuyu.+ Chivumbulutso 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo kumwamba kunakanganuka ngati mpukutu umene akuupinda,+ ndipo phiri lililonse ndi chilumba chilichonse zinachotsedwa m’malo awo.+
4 Makamu onse akumwamba adzawola.+ Kumwamba kudzapindidwa ngati mpukutu wolembapo.+ Makamu onse akumwambawo adzafota ngati mmene masamba amafotera pamtengo wa mpesa n’kuthothoka, ndiponso ngati mmene nkhuyu yonyala imathothokera mumtengo wa mkuyu.+
14 Ndipo kumwamba kunakanganuka ngati mpukutu umene akuupinda,+ ndipo phiri lililonse ndi chilumba chilichonse zinachotsedwa m’malo awo.+