Luka 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iye adzalamulira monga mfumu panyumba ya Yakobo kwamuyaya, moti ufumu wake sudzatha konse.”+ Aheberi 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iyeyu wakhala wotero, osati malinga ndi zofunika za chilamulo, chimene chimadalira zinthu za padziko lapansi,+ koma malinga ndi mphamvu imene imapatsa moyo wosakhoza kuwonongeka.+ Aheberi 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yesu Khristu ali chimodzimodzi dzulo ndi lero, ndiponso mpaka muyaya.+
16 Iyeyu wakhala wotero, osati malinga ndi zofunika za chilamulo, chimene chimadalira zinthu za padziko lapansi,+ koma malinga ndi mphamvu imene imapatsa moyo wosakhoza kuwonongeka.+