Mateyu 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Tsopano tamverani! Mulungu wachoka n’kukusiyirani+ nyumba* yanuyi.+ Aefeso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+ Akolose 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+
14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+
14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+