1 Petulo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chofanana ndi chingalawacho chikupulumutsanso inuyo tsopano.+ Chimenechi ndicho ubatizo, (osati kuchotsa litsiro la m’thupi, koma kupempha chikumbumtima chabwino kwa Mulungu,)+ mwa kuukitsidwa kwa Yesu Khristu.+
21 Chofanana ndi chingalawacho chikupulumutsanso inuyo tsopano.+ Chimenechi ndicho ubatizo, (osati kuchotsa litsiro la m’thupi, koma kupempha chikumbumtima chabwino kwa Mulungu,)+ mwa kuukitsidwa kwa Yesu Khristu.+