Aroma 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndani adzawatsutsa? Khristu Yesu ndiye amene anafa, zoonadi, amenetu anaukitsidwa kwa akufa. Iye ali kudzanja lamanja+ la Mulungu, ndipo amatilankhulira mochonderera kwa Mulunguyo.+ Akolose 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe, ngati munaukitsidwa+ limodzi ndi Khristu, pitirizani kufuna zinthu zakumwamba,+ kumene Khristu wakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+
34 Ndani adzawatsutsa? Khristu Yesu ndiye amene anafa, zoonadi, amenetu anaukitsidwa kwa akufa. Iye ali kudzanja lamanja+ la Mulungu, ndipo amatilankhulira mochonderera kwa Mulunguyo.+
3 Komabe, ngati munaukitsidwa+ limodzi ndi Khristu, pitirizani kufuna zinthu zakumwamba,+ kumene Khristu wakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+