Yohane 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukakhululukira munthu amene wachita tchimo,+ ndiye kuti Mulungu wamukhululukira kale. Koma mukapanda kukhululukira munthu amene wachita tchimo, ndiye kuti Mulungu sanamukhululukire.”+
23 Mukakhululukira munthu amene wachita tchimo,+ ndiye kuti Mulungu wamukhululukira kale. Koma mukapanda kukhululukira munthu amene wachita tchimo, ndiye kuti Mulungu sanamukhululukire.”+