Deuteronomo 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi. Mateyu 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti kulikonse kumene awiri kapena atatu asonkhana m’dzina langa,+ ine ndidzakhala pakati pawo.”+ Machitidwe 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chotero iwo anapitiriza kulabadira zimene atumwiwo anali kuphunzitsa. Iwo anali kugawana zinthu,+ kudya chakudya+ komanso kupemphera.+ Machitidwe 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’chipinda cham’mwamba+ mmene tinasonkhanamo, munali nyale zambiri ndithu.
12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi.
20 Pakuti kulikonse kumene awiri kapena atatu asonkhana m’dzina langa,+ ine ndidzakhala pakati pawo.”+
42 Chotero iwo anapitiriza kulabadira zimene atumwiwo anali kuphunzitsa. Iwo anali kugawana zinthu,+ kudya chakudya+ komanso kupemphera.+