Genesis 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Mulungu anati: “Tiyeni+ tipange munthu m’chifaniziro chathu,+ kuti akhale wofanana nafe.+ Ayang’anire nsomba zam’nyanja ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga, komanso nyama zoweta. Ayang’anirenso dziko lonse lapansi ndi nyama zonse zokwawa padziko lapansi.”+ Genesis 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo cholengedwa chilichonse chamoyo cha padziko lapansi, cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, chilichonse chokwawa padziko lapansi, ndi nsomba zonse za m’nyanja, zizikuopani. Tsopano ndapereka zonsezi m’manja mwanu.+
26 Kenako Mulungu anati: “Tiyeni+ tipange munthu m’chifaniziro chathu,+ kuti akhale wofanana nafe.+ Ayang’anire nsomba zam’nyanja ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga, komanso nyama zoweta. Ayang’anirenso dziko lonse lapansi ndi nyama zonse zokwawa padziko lapansi.”+
2 Ndipo cholengedwa chilichonse chamoyo cha padziko lapansi, cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, chilichonse chokwawa padziko lapansi, ndi nsomba zonse za m’nyanja, zizikuopani. Tsopano ndapereka zonsezi m’manja mwanu.+