Luka 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano atumwiwo anauza Ambuye kuti: “Tiwonjezereni chikhulupiriro.”+ Luka 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndikukuuzani, Iye adzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa iwo mwamsanga.+ Koma, Mwana wa munthu akadzafika, kodi adzapezadi chikhulupiriro padziko lapansi?” Agalatiya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso, mfundo yakuti palibe munthu amene angaonedwe ngati wolungama+ ndi Mulungu mwa chilamulo ndi yoonekeratu, chifukwa “wolungama adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.”+
8 Ndithu ndikukuuzani, Iye adzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa iwo mwamsanga.+ Koma, Mwana wa munthu akadzafika, kodi adzapezadi chikhulupiriro padziko lapansi?”
11 Komanso, mfundo yakuti palibe munthu amene angaonedwe ngati wolungama+ ndi Mulungu mwa chilamulo ndi yoonekeratu, chifukwa “wolungama adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.”+