Genesis 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo Nowa anachita zonse motsatira zimene Mulungu anamulamula. Anachitadi momwemo.+