Oweruza 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita nthawi, mkaziyo anabereka mwana wamwamuna ndipo dzina lake anamutcha kuti Samisoni.+ Mnyamatayo anali kukula, ndipo Yehova anapitiriza kumudalitsa.+
24 Patapita nthawi, mkaziyo anabereka mwana wamwamuna ndipo dzina lake anamutcha kuti Samisoni.+ Mnyamatayo anali kukula, ndipo Yehova anapitiriza kumudalitsa.+