1 Samueli 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ anadziwa kuti Samueli ndiye anali wovomerezeka kukhala mneneri wa Yehova.+
20 Tsopano Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ anadziwa kuti Samueli ndiye anali wovomerezeka kukhala mneneri wa Yehova.+