Yohane 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ine ndikudziyeretsa chifukwa cha iwo, kuti iwonso ayeretsedwe+ ndi choonadi. Aheberi 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akuchititsa anthu amene akuyeretsedwa kukhala angwiro kwamuyaya,+ kudzera mu nsembe imodzi yokha basi.+
14 Iye akuchititsa anthu amene akuyeretsedwa kukhala angwiro kwamuyaya,+ kudzera mu nsembe imodzi yokha basi.+