Miyambo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Phunzitsa mwana m’njira yomuyenerera.+ Ngakhale akadzakalamba sadzapatukamo.+