Mateyu 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma ndikukuuzani kuti, kuyambira tsopano sindidzamwanso chakumwa ichi chochokera ku mphesa kufikira tsikulo pamene ndidzamwa chatsopano limodzi ndi inu mu ufumu wa Atate wanga.”+ Chivumbulutso 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+
29 Koma ndikukuuzani kuti, kuyambira tsopano sindidzamwanso chakumwa ichi chochokera ku mphesa kufikira tsikulo pamene ndidzamwa chatsopano limodzi ndi inu mu ufumu wa Atate wanga.”+
2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+