-
Machitidwe 27:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Choncho anadula anangula ndi kuwagwetsera m’nyanja. Anamasulanso zingwe zomangira nkhafi zowongolera. Atakweza m’mwamba nsalu ya kutsogolo ya ngalawa, analunjika kugombelo.
-